Chitsimikizo cha chinsinsi

Kakakhala kuti nkoyamba kulembetsa, mufunsidwa kuti mulembetse dzina lanu, imelo ndi zinthu zina zokhuza inuyo. Dzina ndi imelo yanu ndi zomwe zikuthandizireni kuti muyambe maphunziro anu, zofunikira zina komanso mayeso kuti muthe kulandira chiphaso cha maphunziro anu. Zinthu zina ndizothandizira pa chiwerengero cha anthu omwe atenga maphunzirowa.

Bungwe lotchedwa LHL International ndi lomwe lizisunga zonse zomwe inu mudzalembetsa za mmenemu. Ndipo amene aziyang’anira zolemberazi mu sisitimu yonseyi ndi a Plott AS kuonesetsa kuti palibe amene akuziona, komanso kuthana ndi zovuta zina zili zonse zomwe zingakhuze zolemberazi. Ngati mukufuna kuchotsa zonse zomwe munalembetsa mu dongosolo umu, tumizani imelo ku post@lhlinternasjonal-kurs.no

Malamulo a ma kukizi a inteneti

Mukafuna kutipeza pa tsamba ili “lhlinternasjonal-kurs.no”, kapena ma tsamba ogwirizana ndi tsamba limeli, pali malo ena amene amasunga uthenga kapena zolemba zina zochepa pa kompyuta yanu zotchedwa kukizi -“cookies”

“Cookies” ndi zinthu zimene zimagwiritsidwa ntchito mwa zina monga kupeza mauthenga ena akagwiritsidwe ntchito pa tsamba la itaneti “website” ndipo ndi njira yimodzi yodziwira kuti kodi ndi mbali ziti zimene ophunzirawo amakonda kuyang’ana kapena kugwiritsa ntchito pa maphunziro awo. Ndipo zotsatira zake ndikusintha kachitidwe kazinthu ka iwo ogwiritsa ntchito tsamba la intanetiyi ncholinga choti ogwiritsa ntchitoyo asamavutike.

Makina osanthula a google

Timagwiritsa ntchito makina a google kuti tidziwe mmene masamba a intaneti akugwiritsidwira ntchito. Timapeza masamba a pa intaneti amene akugwiritsidwa ntchito pafupipafupi, kumene anthu amene akugwiritsawo ntchitowo akuchokera, komanso nthawi imene masambaso anthu amakonda kuwatsekula ndi zina zotero.

Makina asanthulilawa ndi tsamba la pa intaneti limene limayendetsedwa ndi a Google. Makina osanthulila a google amagwiritsa ntchito kukizi kuti ipeze mmene anthu akugwiritsira ntchito tsamba la pa itaneti. Zinthu zimene kukizi amapezazi kuchokera ku masamba a paitaneti amenewa, komanso njira za pa itaneti zimenezi zimatumizidwa ku Gugu ndipo zimakasugidwa kumalo osungira zinthu za pa itaneti ku dziko la USA.

Google amatha kutumiza ziwerengero zimenezi kwa anthu ena motsatira malamulo ngati zikufunika kutero, kapena ngati anthuwo amasamalira ziwerengerozo malo mwa Google yo.

Mmene mungapewere ma kukizi

Ngati simukufuna ma kukizi amenewa, mungapite pamalo amene mumalowera pa tsamba la intaneti ndikusitha kuti musamalandire kapena kutumiza zinthu nthawi iliyonse imene ikufuna koma kuti inuyo mwini wake mudzichita kusakha zimene mukufuna kutumiza kapena kulandira. Komabe ngati mwasakha kuti kukizi asamagwire ntchito pamene muli pa tsamba la intaneti dziwani kuti zinthu zina sizimagwira bwino ntchito yake ndipo simumakhala ndi mwayi wa zinthu zonse zimene zili pa tsamba la itaneti limeneli.

Privacy statement

When you register for the first time, you will be asked to register your name, e-mail and some information about you. Names and e-mails are used to give you access to courses, tasks and tests and to provide you with a personal course certificate. The other information is used for statistical purposes.

LHL International is responsible for managing the data. The system supplier Plott AS is the data processor and supplier of security, operation and maintenance of the solution. If you later want your account deleted, send an e-mail to post@lhlinternasjonal-kurs.no

Cookie Policy

When you visit us at “lhlinternasjonal-kurs.no”, or through links related to this, the site stores certain information on your computer in small text files, called cookies.

Cookies are used, among other things, to give users access to various functions on the website, and are a common method to see which pages users visit. The information is used to improve the user experience and further develop the website.

Google Analytics

We use Google Analytics to analyze the use of the websites. We get information about which pages are most visited, where the users come from, at what times the pages are most visited, etc.

Google Analytics is a web analytics service provided by Google, Inc. (“Google”). Google Analytics uses cookies to analyze how users use the website. The information generated by such a cookie using the relevant website, including your IP address, is sent to Google and stored on servers in the USA.

Google may transfer the statistics to third parties if required to do so by law, or in cases where third parties process the information on behalf of Google.

How to avoid cookies

If you do not want to accept our use of cookies, you can go in and withdraw your consent by changing the settings in the browser so that you either block cookies from being downloaded automatically, or that you get a choice to download each one cookie. Cookies that have been downloaded previously can also be deleted by the browser.

However, we point out that if you choose to block cookies, this may mean that some services on our website do not work optimally, or that you do not have access to all parts of our website.